
Zodabwitsa zomwe zidachitika pambuyo pakuphedwa Imam Husain(a) 4

Mukuyang’ana kwa mashia akunena kuti Mtumiki wawo Muhammad (s.a.w.w) ndi yemweyo yemwe Ahlusunnah ali nawo. Kusonyeza kuti Mtumiki wawo onsewa ndi Muhammad bin Abdullah.

Mipatuko iwiri imeneyi (Shia ndi Sunni) ndiofanana muzikhulupiriro zokhudza Mtumiki (s.a.w.w). Onse amakhulupirira kuti Mtumiki ndi: - otumizidwa ndi Mulungu. - Mtumiki omaliza. - Munthu...

Ahlusunnat ali a mipatuko inayi:1- Hannafi 2- Hanbali 3 –Shafi ndi Maliki. Kuchokera mmipatuko imeneyi pakupezekanso mipatuko ina ing’ono ing’ono yomwe ikuchokera mmenemu monga mmpatuko wa...

Maulawi Abdulrahim (sunni) akunena kuti: “Pakati pa mawahhabi ndi sunni pali kusiyana kwambiri pakuganiza ndizikhulupiriro....Mau anga kwa asilamu asunni anzanga ndi oti mpatuko...

Shaikh wapa Azhar adanena kuti: Mubarrak pofuna kusangalatsa Zionists adali kutilimbikitsa kuti tizigwiritsa ntchito mafatwa achiwahhabi osochera ndikumazetsa kusiyana maganizo pakati pa...

Kupempha chithandizo kwa Mulungu kudzera mwa Atumiki ndi anthu oyera sizikutanthauza kuti anthu amenewa tikuwayika pamalo ofanana ndi Mulungu ayi, koma kuti chifukwa cha ulemelero...

Munthu amene waikira umboni za umodzi wa Mulungu ndi utumiki wa Muhammad ndinso ndikuimika mapemphero, kupereka chopereka, kusala chakudya mmwezi wa Ramadhan ndikupita ku hajji ndi msilamu...

Muchisilamu muli nkhani yoti msilamu wina aliyense ali ndi ufulu (Haqq) kwa msilamu nzake. Angakhale zinyamanso zili ndi ufulu kwa munthu mwachitsanzo ngati munthu ali ndi chinyama chomwe...

Monga momwe tidalongosolera kukumana kwadutsa pankhani ya mapata achipembedzo cha chisilamu kuti ndi kukhulupirira za umodzi wa Mulungu, Utumiki wa Muhammad ndi Kuuka kwa akufa.

Mulungu povumbulutsa Muhammad (s.a.w.w) kukhala Mtumiki adapereka mtendere waukulu kwa mtundu wa anthu kuti achoke mu umbuli ndi kuponderezedwa. Mtumiki ndi ntchito yake yaikulu yomwe...

Hz;Nuh (as)’ın Kısaca Hayatını Kur’an ışığında anlatmaya çaılışarak o dönemdeki toplumsal sıkıntıları tahlil ederek bu dönemdeki toplumun yaşadıklarına benzerlik yönlerinide ele aldık.

Liu lotiأمّيّ muchiluya likuchokera pa mau awiri أمّ (mai) kapena أمّة (Gulu). Anthu otanthauzira Quran adati Ummiyy kutanthauza kusawerenga monga momwe adabadwira mwa mai ake ndipo...

“ Ngati utsogoleri wadziko lapansi udakapatsidwa mmanja mwa Muhammad, dziko lapansi lidakakhala pachisangalalo. Chisilamu chidakatsogolera dziko lonse ku kupambana ndikuthetsa mavuto onse.”

Kodi zikhulupiriro zimenezi ndizoona? Mtumiki yemwe Mulungu akumutcha kuti Rahmatulilialamina, oti kungo mwalira alibenso phindu? Ndichifukwa chiyani ife mu athana pambuyo pakuvomereza...

Muhammad Abdul Wahhabi adanena mubukhu lake la Tauhid kuti kupereka dzina la Abdul posakhala Mulungu ndi shrik, pachifukwachi iye adanena kuti Hazrat Adam ndi mkazi wake ndi mamushrik...

Fatima ndi mwana wa Mtumiki (s.a.w.w). Iye ali maina opatsidwa (laqab) ambiri monga: Zahra, Maridhiyya, Batuli, Muhditha ...

Fatima ndi mwana wa Mtumiki (s.a.w.w). Iye ali maina opatsidwa (laqab) ambiri monga: Zahra, Maridhiyya, Batuli, Muhditha.Tikafuna kukamba za upamwamba wake pamaso pa bambo ake (s.a.w.w)...

Ma wahhabi su’udi mchaka cha 1220 kapena 1221 adachita chiwembu nzinda wa Madina ndipo adauzungulira kwa chaka chimodzi ndi theka ndipo mapeto ake nzindawu udakhala mmanja mwawo.

Ma wahhabi su’udi mchaka cha 1220 kapena 1221 adachita chiwembu nzinda wa Madina ndipo adauzungulira kwa chaka chimodzi ndi theka ndipo mapeto ake nzindawu udakhala mmanja mwawo.