Kusiyana kwa Chiwahhabi ndi Sunni:Gawo1
Ahlusunnat ali a mipatuko inayi:1- Hannafi 2- Hanbali 3 –Shafi ndi Maliki. Kuchokera mmipatuko imeneyi pakupezekanso mipatuko ina ing’ono ing’ono yomwe ikuchokera mmenemu monga mmpatuko wa chiwahhabi omwe umazinena kuti umatsatira zikhulupiriro za Hanbal
Ahlusunnat ali a mipatuko inayi:1- Hannafi 2- Hanbali 3 –Shafi ndi Maliki.
Kuchokera mmipatuko imeneyi pakupezekanso mipatuko ina ing’ono ing’ono yomwe ikuchokera mmenemu monga mmpatuko wa chiwahhabi omwe umazinena kuti umatsatira zikhulupiriro za Hanbali.
| Attachment | Size |
|---|---|
| 43 MB |
Add new comment