KODI MA SHIA ALI NDI MULUNGU WINA POSAKHALA MULUNGU MMODZI YU
NANGA KODI MA SHIA ALIE A.S AMATENGA KUKHALA MULUNGU KODI NDI ZOONA ?
MU ULALIKI UWU UKUTIPHUZINSA KUTI ALIE A.S SANALI MULUNGU NDITHU KOMA KUTI ANALI MA IMAMU KAPENA MTSOGOLERI WA MULUNGU NDITHU , KOMANSO NGATI AMAPANGA ZODABWINSA KOMA NDI CHIFUNILO CHA CHA ALLAH NDITHU BANSI
| Attachment | Size |
|---|---|
| 60.8 MB |
Add new comment