KODI MA SHIA ALI NDI MULUNGU WINA POSAKHALA MULUNGU MMODZI YU
NANGA  KODI  MA SHIA ALIE A.S AMATENGA KUKHALA MULUNGU KODI  NDI ZOONA ? 
MU ULALIKI UWU UKUTIPHUZINSA KUTI ALIE A.S SANALI MULUNGU NDITHU KOMA KUTI ANALI MA IMAMU KAPENA MTSOGOLERI WA MULUNGU NDITHU , KOMANSO NGATI AMAPANGA ZODABWINSA KOMA NDI CHIFUNILO CHA CHA ALLAH NDITHU BANSI
| Attachment | Size | 
|---|---|
|  12444-f-chichwa.mp4 | 60.8 MB | 
Add new comment