Sahaba 1
Swahaba amapanga zomwe walamulira (fatwa) ndipo ngati angalakwitse ndiye kuti achita Ijtihad ndipo ali ndithawab imodzi. Pachifukwachi tilibe ufulu ofufuza za iwo. Munthu yemwe angafufuze za kulakwa kwa Swahaba ndikafir.
| Attachment | Size |
|---|---|
| 39.21 MB |
Add new comment