Zolankhula za Imam Ali (a.s) ndizothandiza kwambiri pagulu la anthu (society) chifukwa zikunena mfundo zoyenera munthu kuzitsatira kuti moyo wake uyende bwino.
Add new comment