KUNYOZEDWA KWA ASILAMU NDI INA MWA NEWSPAPER YAKU FRANCE
KUNYOZEDWA KWA ASILAMU NDI INA MWA NEWS PAPER YAKU FRANCE

News paper  ina  yaku  France  yotchedwa  valeurs Actuel  yafalitsa  uthenga  onyoza  Asilamu  ndikunena  kuti  ayenera  kuthamangitsidwa  mdzikomo  ndipo  nkhani  imeneyi ali  nayo  kaliki-liki 
  
pofuna  kulimbana  ndi  Chisilamu, akufalitsa  uthenga  wakuopsa  kwa  Chisilamu  pagulu  la  anthu (society) ndikunyoza  azimayi  ovala  hijabu
Add new comment