Zoyenera kuchita mutsiku la Eid Ghadir 2
Mutsiku la Eid Ghadir, Mulungu akumukhululukira okhulupilira wamamuna komanso wamkazi machimo a zaka 60, kusala mutsiku limeneli kukufanana ndikusala komwe munthu angasale umoyo wake onse, kusala mutsikuli kufanana ndi Haj zokwana 100 komanso Umurah zokwana 100…
| Attachment | Size |
|---|---|
| 60.36 KB |
Add new comment