Mwezi wa Ramadhan
Malamulo onse achisilamu adakhazikidwa ndicholinga choti munthu akhale pa mtendere ndi ufulu, ngakhale malamulo a Mulungu omwe anthu ena chifukwa cha zolinga ndi matenda omwe alinawo, akusemphana ndi kumatsutsana nawo, zomwe zili zodandaulitsa kwambiri.
| Attachment | Size |
|---|---|
| 55.11 MB |
Add new comment