Kodi tidzayankha chiyani mu usiku wathu oyamba m’manda: Imam (mtsogoleri) wathu ndi ndani?-2
Imam Ali (A.S) pankhondo ya Siffin adanena kuti: أنا النبأ العظیم الذی فی اختلفتم و فی خلافتی تنازعتم “Ine ndiye nkhani yaikulu ija yomwe inu mudasemphana komanso mudakangana pokhudzana ndi ulowa m’malo wanga
| Attachment | Size |
|---|---|
| 28.89 MB |
Add new comment