Mitundu ya Ibadah (1)
Anthu ena akumugwadira Mulungu ndi cholinga chofuna mtendere wake omwe ali malonda, ena akumugwadira Mulungu chifukwa chowopa moto wa Mulungu, omwe ali mapemphero a akapolo ndipo ena akumugwadira Mulungu chifukwa chongomuthokoza, omwe ali mapemphero a amfulu….
| Attachment | Size |
|---|---|
| 22.72 MB |
Add new comment