Kuonongedwa kwa Quran 4
Mashia samangovomereza hadith ina iliyonse yomwe ikupezeka mmabuku amahadith monga Usulul Kafi, zasiyana ndi ena omwe amawatcha mabuku amadith kuti ndi a swahih, mashia amatha kuikana hadith angakhale yamu usulul kafi ngati sanadi yake sili yovomerezeka.
| Attachment | Size |
|---|---|
| 19.04 MB |
Add new comment