Wahabiyyat 10
- Chiyambi cha Chiwahhabi. Mpingo wa Chiwahhabi upatenga dzinali kuchokera kwa Muhammad mwana wa Abdul Wahhabi. Iye adabadwa mchaka cha 1115 hijr mudera la Uyayinah lomwe ndi dera limodzi mwa madera a nzinda wa Najdi.
| Attachment | Size |
|---|---|
| 29.6 MB |
Add new comment