Mtumiki adanena kuti nthawi ya Imam Zaman umoyo wudzakhala wapamwamba kuposa nyengo zonse ndipo chuma chidzapita patsogolo komanso nthaka sidzasiya kanthu osakameretsa.
Add new comment