Utumiki:Gawo 25 (B)
Mipatuko iwiri imeneyi (Shia ndi Sunni) ndiofanana muzikhulupiriro zokhudza Mtumiki (s.a.w.w).
Onse amakhulupirira kuti Mtumiki ndi:
- otumizidwa ndi Mulungu.
- Mtumiki omaliza.
- Munthu osankhidwa ndi Mulungu kudzaongola anthu.
Attachment | Size |
---|---|
![]() | 29.2 MB |
Add new comment