KUNYOZEDWA KWA ASILAMU NDI INA MWA NEWSPAPER YAKU FRANCE
KUNYOZEDWA KWA ASILAMU NDI INA MWA NEWS PAPER YAKU FRANCE

News paper ina yaku France yotchedwa valeurs Actuel yafalitsa uthenga onyoza Asilamu ndikunena kuti ayenera kuthamangitsidwa mdzikomo ndipo nkhani imeneyi ali nayo kaliki-liki
pofuna kulimbana ndi Chisilamu, akufalitsa uthenga wakuopsa kwa Chisilamu pagulu la anthu (society) ndikunyoza azimayi ovala hijabu
Add new comment