Umtsogoleri wa Mulungu mukuyang,ana Mashia
chidule cha nkhani ya umumu ndi choti pa umtsogoleri wa pambuyo pa mtumiki muhammadi kuti kodi umtsogoleri akuyenela kusankha anthu or mtumiki mwini wake mtumiki yu ? umumu zikutanthaudzanso kuti azathu asunni amati umtsogoleri ndi nthambi chabe ya chis
chidule cha nkhani ya umumu ndi choti pa umtsogoleri wa pambuyo pa mtumiki muhammadi kuti kodi umtsogoleri akuyenela kusankha anthu or mtumiki mwini wake mtumiki yu ? umumu zikutanthaudzanso kuti azathu asunni amati umtsogoleri ndi nthambi chabe ya chisilamu pomwe azathu achi shia amakhulupilila zoti mapata achisilamu komanso amakhulupila nso kuti kuti uimama akuyenera kunsankha mwiniwake allah or mtumiki muhammadi s.a.a w . pomwe azathu achisunni amakhulupilila kuti atha kunsakha anthu ngati mwa member of parliament.
Attachment | Size |
---|---|
12260-f-chichwa.mp4 | 36.82 MB |
Add new comment