Ulemelero wa Imam Husein (A.S) Part-1
Mngelo Jibril adafika kwa mtumiki (s.a.a.w) ndipo adamusangalatsa mtumiki Muhammad (s.a.a.w) pomuwuza kuti posachedwapa mwana wako wamkazi Fatima (a.s) azakhala ndi mwana yemwe adzaphedwa ndi Ummah wako pambuyo pako.
Attachment | Size |
---|---|
![]() | 29.4 MB |
Add new comment