Ndipo ndithudi Abbas kwa Mulungu ali ndi ulemelero ndi malo apamwamba omwe anthu onse ophedwa mu njira ya Mulungu adzakumbira ndi kulakalaka kuti atakhalaa nawo pa tsiku lomaliza
Add new comment