Zoyenera kuchita mutsiku la Eid Ghadir
Mutsiku la Eid Ghadir, Mulungu akumukhululukira okhulupilira wamamuna komanso wamkazi machimo a zaka 60, kusala mutsiku limeneli kukufanana ndikusala komwe munthu angasale umoyo wake onse, kusala mutsikuli kufanana ndi Haj zokwana 100 komanso Umurah zokwana 100…
Attachment | Size |
---|---|
![]() | 1.83 MB |
Add new comment