Ma Ayah olozera za Imam Mahdi (AJ)-2
Tikamawona mu Quran, tikupezamo kuti muli ma Ayah ena omwe uthenga wake mpakana pano siudachitike, kapena zomwe zanenedwazo sizidachitike. Zomenezi zidzachitika nthawi ya Imam Mahdi (AJ)
Attachment | Size |
---|---|
![]() | 439.5 KB |
Add new comment