Chisilamu chamangidwa Pakuphweka ndi Kukwanitsa kwathu

Mulungu akulankhula mu Quran kuti: \"Ife sitimamukakamiza munthu pokha pokha ndi kukwanitsa kwake\" Malamulo a Mulungu amasintha potengera ndi m\'menenso munthu aliri. Malamulo a Mulungu akumangidwanso panzeru. Izi zili choncho ngati munthu wamudziwa Mulungu kuti ndi wanzeru komanso waluntha.

AttachmentSize
File 8fbbc4ab3edecf198792d317e937494b.mp46.65 MB

Add new comment