Kuipa kosapanga Taqiyyah:kuphedwa.kuikidwa pamavuto pamodzi ndi anthu ena.Ngati munthu angapange Taqiyyah mopsola muyezo ndiye kuti zotsatira zabwino za Taqiyyah zimapita pachabe.
Add new comment