UTUMIKI 10
- Kodi nzeru za munthu zingathe kuvomereza kuti Atumiki ayenera kukhala osalakwa kapena ayi? Kodi Mtumiki akakhala ochimwa awaletsa ena bwanji kuti asalakwe? ( Monga Mtumiki ndi mwana yemwe mai ake adamubweretsa kwa iye kuti amuletse kudya tende kwambiri).
Attachment | Size |
---|---|
0b5486dc94ded458f71197b299963899.mp4 | 14.31 MB |
Add new comment