Atsikana achi Shia ku London aonetsa kufunikira kwa mapemphero.

Atsikana  achi Shia ku London  aonetsa  kufunikira  kwa  mapemphero

 

.
Atsikana  a gulu  la shia  aonetsa  kufunikira  kwa  mapemphero   mu nthawi  yake  poiyimitsa  zokwera  zawo  ndikuyamba  kupemphera  mphepete  mwa  nseu  popanda  mantha.
Atsikanawa  pofuna  kulimbikitsana  nkhani ya  mapemphero  amakhala  akunena  kuti:  “ukamva akunena  athana, kwina kulikonse  komwe  uli,  thamangira  kumaphemphero  angakhale  utakwera  galimoto  lako  uli  pakati  panseu wa nzinda  wa  London, uyenera  kuimika  galimoto  lako  pambali,  kupanga  udthu   ndikuima  kupemphera.”
Inde  ziyenera  kutero  ndithu  chifukwa  mapemphero  ndichinthu  chofunikira  kwambiri  mu umoyo wa  munthu.
Inu  atsikana  athu  tengerani  chitsanzo  pankhaniyi.
Khalani  opemphera  nthawi  zonse  ndi  munthawi  yake.
 

 

Add new comment