Zionetsero za Husain (a) mu Quran 3
Zionetsero za Husain (a) mu Quran 3
((و لا تقتلوا النفس التى حرم الله الا بالحق)) (الاسراء / 33)
Mulungu akunena kuti ((Musamuphe munthu yemwe ali oletsedwa kuphedwa pokha pokha ngati pali chilungamo choti aphedwe)).
Imam Swadiq (a) adanena kuti tanthauzo la munthu yemwe ali oletsedwa kuphedwa ndi Husain yemwe adamupha pakati pa banja lake.
Add new comment