Zionetsero za Husain (a) mu Quran2.
Zionetsero za Husain (a) mu Quran2.
فنظر نظرة فى النجوم * فقال إنى سقي (الصافات / 88 - 89)
Mtumiki Ibrahim (a) adayang’ana nyenyezi ndipo adati Ine ndikudwala (choncho sindibwera nanu kunsonkhanawo).
Imam Swadiq (a) zokhudzana ndi ayayi adati: Hazrat Ibrahim chifukwa cha mavuto omwe adzamugwere Husain (a) adaganizira ndikunena kuti: chifukwa cha mavuto omwe adzamugwere Husain (a) ine ndadwala nawo.
(Al’awalim:volume 17,tsamba 98)
Add new comment