Zionetsero za Husain (a) mu Quran-kulira kwa kumwamba ndi pansi pano 1.
Zionetsero za Husain (a) mu Quran-kulira kwa kumwamba ndi pansi pano 1.
Munthu wina adanena kuti: Tsiku lina Amir muminina Ali (a) adakhala mu nzikiti ndipo adali kuwerenga aya yomwe ikuti: ((kumwamba ndi pansi pano sizidawalilire iwo ndipo mpata sudapatsidwe kwa iwo)) zilichoncho adatulukira Husain (a), Ali adati: e! inu Asilamu dziwani kuti uyu Husain adzaphedwa ndipo kumwamba ndi pansi pano zidzamulilira.
(kamil ziyarat,tsamba 125).
Add new comment