Zoyenera kuchita mutsiku la Eid Ghadir (Dua)
Munthu yemwe angapemphere Swalat ya tsiku la Eid Ghadir ndikuwerenga duwayi pambuyo pa Swalat, akupeza malipiro (Thawab) ngati adali limodzi ndi mtumiki ndipo adavomereza za utsogoleri wa Imam Ali (A.S) pa Ghadir Khum. Tsiku la Ghadir likumukumbutsa munthu phangano la Mulungu lomwe adalipanga panthawi yolengedwa ndipo munthuyo mutsikuli akutsatira utsogoleri wa Imam Ali (A.S)
Attachment | Size |
---|---|
13c8e5d3167dd253d5706852fc3fb843.mp4 | 25.17 MB |
Add new comment