Madzi a Mudhwaf

Madzi a Mudhwaf ndi madzi monga; Madzi a mandimu, a mchere, ma Juice, Mkaka, a Suger, Msuzi ndi zina zotero. Mwachidule madzi omwe sitimagwilitsira ntchito kuyeletsa zinthu zina. Madziwa ali ndi malamulo atatu: 1) Ngakhale kuti ndi oyere muchilengedwe chake koma sitingathe kuyeletsera zinthu zina pofuna kuchotsa Najs. 2) Amadetsedwa onse chongokumana ndi Najs ngakhale atachuluka bwanji. 3) Ndizosatheka Kusambira kapena kupangira Wudhu.

AttachmentSize
File 4a0a245deff7d21eaf08cb79df116622.mp47.64 MB

Add new comment