Kuleledwa kwa munthu kudutsira mwa olemekezeka Yesu (A.S)

Mulungu pofuna kumulera munthu kuti akhale wa Umulungu ndikuti azindikire mphamvu zake, pali njira zosiyana siyana zomwe adayika. Zina mwa njira zodziwira mphamvu ya Mulungu ndi kupezeka kwa olemekezeka Yesu ndi Mayi Maria mtendere ndi madalitso a Mulungu ukhale kwa awiriwa. Koma zinthu zomwe zidzakhala zikuchitika mwa iwo, zisadzamutanthauzire munthu kuti Yesu ndi Mulungu kapena mwana wa Mulungu.

AttachmentSize
File 4a7d5aa55a31ced78ce6686386fdd77d.mp426.92 MB

Add new comment