Chozizwitsa (Mujizah) ndi chodabwitsa chomwe Mtumiki amachita ndipo amawauza anthu ena kuti ngati angathe apange ngati chomwecho koma iwo amalephera.
Add new comment