Utumiki:Part 13
Pambuyo pakuzindikira anthu oipa kuti Mtumiki omaliza adzabadwa kuchokera kuntundu wa mabani Hashim kubanja la AbdulMutwalib ndi Abdullah komanso Aminah, adafuna kuti kuwala komwe kulipo mwa iwo komwe ndi kuwala kwa Mtumiki omaliza akusowetse.
Attachment | Size |
---|---|
5373eb69df5cdb973cc8ad75b2bd5a31.mp4 | 13.83 MB |
Add new comment