Pankhani yakubwera kwa Mahdi mashia ndi Ahlu sunnat ndiogwirizana maganizo angakhalenso amene sali asilamu za Imam ameneyu zidalembedwa mmabuku awo kuti kumapeto kwa dziko kudzabwera mpulumutsi.
Add new comment