Iye azamenya nkhondo ndi adani ake komanso otsutsana naye. Chifukwa choti pazapezeka magulu ena omwe sadzagwirizana ndizomwe azidzalalikira ndikuitanira iye komanso kukhazikitsa kwake chilungamo.
Add new comment