Utumiki:Part 22 (B)

Ndizodziwika bwino mu history kuti Ali bin Abi Twalib  amadziwa kulemba ndikuwerenga ndipo iye adakulira mnyumba ya Mtumiki ndipo adalibe phunzitsi wina posakhala Mtumiki, tsono Mtumiki yemwe samadziwa kulemba ndikuwerenga adakwanitsa bwanji kumuphunzitsa iye?

AttachmentSize
File 9b1710eafc7d7f5e09c896fc86a04390.mp413.93 MB

Add new comment