Atsikana achi Shia ku London aonetsa kufunikira kwa mapemphero.
Atsikana achi Shia ku London aonetsa kufunikira kwa mapemphero
.
Atsikana a gulu la shia aonetsa kufunikira kwa mapemphero mu nthawi yake poiyimitsa zokwera zawo ndikuyamba kupemphera mphepete mwa nseu popanda mantha.
Atsikanawa pofuna kulimbikitsana nkhani ya mapemphero amakhala akunena kuti: “ukamva akunena athana, kwina kulikonse komwe uli, thamangira kumaphemphero angakhale utakwera galimoto lako uli pakati panseu wa nzinda wa London, uyenera kuimika galimoto lako pambali, kupanga udthu ndikuima kupemphera.”
Inde ziyenera kutero ndithu chifukwa mapemphero ndichinthu chofunikira kwambiri mu umoyo wa munthu.
Inu atsikana athu tengerani chitsanzo pankhaniyi.
Khalani opemphera nthawi zonse ndi munthawi yake.
Add new comment