KUPANDA ULEMU KWA WAHABI POLANKHULANA NDI MASHIA.
.
KUPANDA ULEMU KWA WAHABI POLANKHULANA NDI MASHIA
Kulankhula ndi maganizo amenewa akuchokera kwa munthu yemwe amazitcha kuti ndi oyitanira anthu muchipembedzo cha Chisilamu, koma tikaonetsetsa tiona kuti khalidwe ndi zochitika zawo ndizosemphana ndi Quran komanso Sunnah ya Mtumiki(s.a.w.w).Kodi inu mungakhulupirire kuti anthu oterewa kukhala oyitanira muchipembedzo cha Chisilamu
Mawahabi nthawi zonse amazitcha kuti ndioyitanira ku Chisilamu koma funso ndilokuti chisilamu chomwe iwowa amachidziwa bwinochi chikuchokera pati? Chifukwa chisilamu chomwe tikuchidziwa ndichomwe chikuphunzitsa chikondi, kukoma mtima,kulemekezana ndi zina zotero,pomwe Mawahabi kwawo ndikupha,nkhanza, udani ndi zotero, choncho tikuona kuti pakati pa chisilamu chimenechi ndichomwe Mtumiki(s.a.w.w) adaphunzitsa palikusiyana kumwamba ndi pansi
Add new comment