Wahabiyat6

{mp3}audio/92.4.30/2659-f-Chichewa-ok{/mp3}

 

Mutu umenewu ndi ofunikira kwambiri kwa munthu wina aliyense makamaka msilamu ofuna njira yeniyeni ya chilungamo ndi cholinga choti azindikire zenizeni za gulu limeneli. Ndipo izi zidzamupangitsa kuti pang’ono ndi pang’ono adzayambe kudziwa choonadi cha chipembedzo cha chisilamu. M’menemu talongosola chiyambi cha gululi ndi gawo lomwe atenga padakali pano pofalitsa chisilamu chabodza, zikhulupiliro zawo, malamulu awo ndi zintchito zawo.

Add new comment