Sheikh Hasan Shahatah akuphedwa momvetsa chisoni ndi ma Wahabiy

Chigulu kapena kuti chinantindi cha anthu ena oyipitsitsa ndi opanda chisoni amudziko la Egypt lomwe lidatumizidwa ndi gulu la Wahabiy la dzikoli, adakhamukira kumwambo wakukumbukira kubadwa kwa Imam Mahdi (A.A.F.S) mu dera la Jizah pafupi ndi mzinda wa Cairo, komwe adapha monvetsa chisoni ndi moipitsitsa munthu olemekezeka yemwe adali mphunzitsi wamkulu pa sukulu yaikulu ya Azhar yemwe adakhala Shia, Sheikh Hasan Shahatah ndi anthu ena okwana anayi (4) omwe adali otsatira Ahalbait (A.S) kunyumba yawo, chifukwa chakuti amakumbukira kubadwa kwa Imam wanthawi yathu ino, yemwe ali Imam Mahdi (A.A.F.S)

Zomwe mukuwona m’musimu ndi magawo ena opweteka a anthu awupanduwa pomenya ndi kupha ma Shia oponderezedwa. Sizikukamizidwa kwa onse kuwonera Filimuyi.

{flvremote}http://www.tvshia.com/farsi/up-files/videos/tvshia.com%20hasan%20shahate...{/flvremote} 

134745516612 اراذل و اوباشی که دانشمند مستبصر مصری شیخ حسن شحاته را به شهادت رساندند / عکس و فیلم + 18

1765qgzb copy اراذل و اوباشی که دانشمند مستبصر مصری شیخ حسن شحاته را به شهادت رساندند / عکس و فیلم + 18

Add new comment