Ndi chifukwa chiyani adani akumanyoza Imam Hadi (a.s)

{mp3}audio/bakhsh-audio/573{/mp3}

 

Ulemelero wa Imam Hadi (a.s) ndi kudabwitsa mu umoyo wake ndi zomwe zikutitsimikizira kuti iye ndi mwana wa Mtumiki Muhammad (a.s) komanso osankhidwa ndi Mulungu kukhala mtsogoleri wa Asilamu munthawi yake.

Add new comment